Genesis 41:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngala zonyalazo zinayamba kumeza ngala 7 zokhwima ndi zazikulu bwinozo.+ Kenako Farao anagalamuka, n’kuona kuti anali maloto.
7 Ngala zonyalazo zinayamba kumeza ngala 7 zokhwima ndi zazikulu bwinozo.+ Kenako Farao anagalamuka, n’kuona kuti anali maloto.