Genesis 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Seti atakhala ndi moyo zaka 105, anabereka Enosi.+ Luka 3:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 mwana wa Enosi,+mwana wa Seti,+mwana wa Adamu,+mwana wa Mulungu.