Esitere 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Moredekai analemba makalatawo m’dzina la Mfumu+ Ahasiwero ndi kuwadinda+ ndi mphete yodindira ya mfumu.+ Atatero anatumiza makalatawo kudzera mwa amtokoma okwera pamahatchi+ aliwiro amene anali kuwagwiritsa ntchito potumikira mfumu. Danieli 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno anabweretsa mwala ndi kutseka pakhomo la dzenjelo. Kenako mfumu inadinda mwalawo ndi mphete yake yodindira ndipo nduna zakenso zinaudinda ndi mphete yawo yodindira, kuti chilichonse chokhudza Danieli chisasinthidwe.+
10 Moredekai analemba makalatawo m’dzina la Mfumu+ Ahasiwero ndi kuwadinda+ ndi mphete yodindira ya mfumu.+ Atatero anatumiza makalatawo kudzera mwa amtokoma okwera pamahatchi+ aliwiro amene anali kuwagwiritsa ntchito potumikira mfumu.
17 Ndiyeno anabweretsa mwala ndi kutseka pakhomo la dzenjelo. Kenako mfumu inadinda mwalawo ndi mphete yake yodindira ndipo nduna zakenso zinaudinda ndi mphete yawo yodindira, kuti chilichonse chokhudza Danieli chisasinthidwe.+