Genesis 47:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Njala itafika poipa kwambiri,+ chakudya chinatheratu m’dziko lonselo. Anthu onse a ku Iguputo ndi a ku Kanani anali ofooka chifukwa cha njalayo.+
13 Njala itafika poipa kwambiri,+ chakudya chinatheratu m’dziko lonselo. Anthu onse a ku Iguputo ndi a ku Kanani anali ofooka chifukwa cha njalayo.+