Genesis 42:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mukabweretse m’bale wanu wamng’onoyo kwa ine kuti ndidzatsimikize kuti si inu akazitape koma anthu achilungamo. Mukadzatero, ndidzakubwezerani m’bale wanuyu, ndipo mudzatha kuchita malonda m’dziko lino.’”+ Genesis 43:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yosefe atakweza maso ake n’kuona mng’ono wake Benjamini, m’bale wake wa mimba imodzi,+ anati: “Kodi uyu ndiye mng’ono wanu amene munali kunena uja?”+ Ananenanso kuti: “Mulungu akukomere mtima+ mwana wanga.”
34 Mukabweretse m’bale wanu wamng’onoyo kwa ine kuti ndidzatsimikize kuti si inu akazitape koma anthu achilungamo. Mukadzatero, ndidzakubwezerani m’bale wanuyu, ndipo mudzatha kuchita malonda m’dziko lino.’”+
29 Yosefe atakweza maso ake n’kuona mng’ono wake Benjamini, m’bale wake wa mimba imodzi,+ anati: “Kodi uyu ndiye mng’ono wanu amene munali kunena uja?”+ Ananenanso kuti: “Mulungu akukomere mtima+ mwana wanga.”