Miyambo 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu opusa akapalamula mlandu amangoseka,+ koma pakati pa anthu owongoka mtima pali mgwirizano.+