Genesis 43:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mulungu Wamphamvuyonse apangitse munthuyo kukuchitirani chifundo,+ kuti akamasule m’bale wanu uja, ndipo mukabwere naye limodzi ndi Benjamini. Koma ngati ndingatayikidwe ana anga, chabwino, zikhale choncho!”+
14 Mulungu Wamphamvuyonse apangitse munthuyo kukuchitirani chifundo,+ kuti akamasule m’bale wanu uja, ndipo mukabwere naye limodzi ndi Benjamini. Koma ngati ndingatayikidwe ana anga, chabwino, zikhale choncho!”+