Genesis 37:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo anapitiriza kuwauza kuti: “Musakhetse magazi ayi.+ Muponyeni m’chitsime chopanda madzichi kutchire kuno, musamuvulaze.”+ Cholinga chake chinali chakuti amupulumutse kwa iwo ndi kum’bwezera kwa bambo ake. Genesis 46:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo ana a Rubeni anali Hanoki, Palu, Hezironi ndi Karami.+
22 Ndipo anapitiriza kuwauza kuti: “Musakhetse magazi ayi.+ Muponyeni m’chitsime chopanda madzichi kutchire kuno, musamuvulaze.”+ Cholinga chake chinali chakuti amupulumutse kwa iwo ndi kum’bwezera kwa bambo ake.