14 Tsopano awa ndiwo atsogoleri a nyumba ya makolo a Aisiraeli. Ana aamuna a Rubeni, yemwe anali mwana woyamba kubadwa wa Isiraeli,+ anali Hanoki, Palu, Hezironi ndi Karami.+ Amenewa ndiwo mabanja a fuko la Rubeni.+
5 Rubeni anali mwana woyamba kubadwa wa Isiraeli.+ Ana aamuna a Rubeni anali: Hanoki+ amene anali kholo la banja la Ahanoki, Palu+ amene anali kholo la banja la Apalu,