Genesis 42:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yosefe atatero, analamula anyamata ake kuti awadzazire tirigu m’matumba awo. Anawalamulanso kuti aliyense am’bwezere ndalama zake pomuikira m’thumba lake.+ Anatinso awapatse kamba wa pa ulendo wawo.+ Anyamatawo anawachitiradi zimenezo.
25 Yosefe atatero, analamula anyamata ake kuti awadzazire tirigu m’matumba awo. Anawalamulanso kuti aliyense am’bwezere ndalama zake pomuikira m’thumba lake.+ Anatinso awapatse kamba wa pa ulendo wawo.+ Anyamatawo anawachitiradi zimenezo.