Genesis 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Kenako Yosefe analamula woyang’anira nyumba yake+ uja kuti: “Udzaze chakudya m’matumba a anthuwa mpaka mlingo woti akhoza kunyamula. Aliyense umubwezere ndalama zake poziika pamwamba pa thumba lake.+
44 Kenako Yosefe analamula woyang’anira nyumba yake+ uja kuti: “Udzaze chakudya m’matumba a anthuwa mpaka mlingo woti akhoza kunyamula. Aliyense umubwezere ndalama zake poziika pamwamba pa thumba lake.+