Genesis 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano Mulungu anati: “Taonani, ndakupatsani zomera zonse zobala mbewu zapadziko lonse lapansi, ndi mitengo yonse yobala zipatso za mbewu+ kuti zikhale chakudya chanu.+ Salimo 72:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Padziko lapansi padzakhala tirigu wambiri.+Pamwamba pa mapiri padzakhala tirigu wochuluka.+Zokolola za mfumu zidzachuluka ngati mitengo ya ku Lebanoni,+Ndipo anthu ochokera mumzinda adzaphuka ngati udzu wa panthaka.+ Mateyu 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kanjere kameneka ndi kakang’ono kwambiri mwa njere zonse, koma kakamera kamakula kwambiri kuposa mbewu zonse zakudimba ndipo umakhala mtengo, moti mbalame zam’mlengalenga+ zimabwera kudzapeza malo okhala munthambi zake.”+
29 Tsopano Mulungu anati: “Taonani, ndakupatsani zomera zonse zobala mbewu zapadziko lonse lapansi, ndi mitengo yonse yobala zipatso za mbewu+ kuti zikhale chakudya chanu.+
16 Padziko lapansi padzakhala tirigu wambiri.+Pamwamba pa mapiri padzakhala tirigu wochuluka.+Zokolola za mfumu zidzachuluka ngati mitengo ya ku Lebanoni,+Ndipo anthu ochokera mumzinda adzaphuka ngati udzu wa panthaka.+
32 Kanjere kameneka ndi kakang’ono kwambiri mwa njere zonse, koma kakamera kamakula kwambiri kuposa mbewu zonse zakudimba ndipo umakhala mtengo, moti mbalame zam’mlengalenga+ zimabwera kudzapeza malo okhala munthambi zake.”+