Ezekieli 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzaibzala pamwamba pa phiri lalitali la ku Isiraeli+ ndipo idzachita nthambi ndi kubereka zipatso+ n’kukhala mtengo waukulu wa mkungudza.+ Mbalame zamitundu yonse zizidzakhala pansi pa mtengowo ndi mumthunzi wa masamba ake.+
23 Ndidzaibzala pamwamba pa phiri lalitali la ku Isiraeli+ ndipo idzachita nthambi ndi kubereka zipatso+ n’kukhala mtengo waukulu wa mkungudza.+ Mbalame zamitundu yonse zizidzakhala pansi pa mtengowo ndi mumthunzi wa masamba ake.+