Salimo 72:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo adzakhala ndi anthu omugonjera kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,+Komanso kuchokera ku Mtsinje*+ kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+ Hoseya 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo adzakhalanso mumthunzi wake.+ Adzabzala mbewu ndipo adzaphuka ngati mpesa.+ Dzina lawo lidzakumbukiridwa ngati vinyo wa ku Lebanoni.
8 Ndipo adzakhala ndi anthu omugonjera kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,+Komanso kuchokera ku Mtsinje*+ kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+
7 Iwo adzakhalanso mumthunzi wake.+ Adzabzala mbewu ndipo adzaphuka ngati mpesa.+ Dzina lawo lidzakumbukiridwa ngati vinyo wa ku Lebanoni.