Genesis 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma uike kapu yanga yasiliva ija pamwamba pa thumba la wamng’onoyo limodzi ndi ndalama zake zogulira tirigu.” Choncho woyang’anira nyumba yakeyo anachita monga mmene Yosefe ananenera.+
2 Koma uike kapu yanga yasiliva ija pamwamba pa thumba la wamng’onoyo limodzi ndi ndalama zake zogulira tirigu.” Choncho woyang’anira nyumba yakeyo anachita monga mmene Yosefe ananenera.+