Genesis 43:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ngati simutilola kupita naye, sititsikirako, chifukwa munthu uja ananenetsa kuti, ‘Musadzayese n’komwe kuonekeranso pamaso panga mukadzalephera kubwera naye m’bale wanuyo.’”+
5 Koma ngati simutilola kupita naye, sititsikirako, chifukwa munthu uja ananenetsa kuti, ‘Musadzayese n’komwe kuonekeranso pamaso panga mukadzalephera kubwera naye m’bale wanuyo.’”+