Genesis 42:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chabwino, ndikuyesani motere kuti ndione ngati mukunena zoona: Simuchoka kuno mpaka mng’ono wanuyo atabwera,+ ndithu pali Farao wamoyo! Genesis 44:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma ife tinati, ‘Sitingathe kutsikira kumeneko. Ngati tikhala naye limodzi mng’ono wathuyu tipitako, chifukwa sitingathe kukaonekeranso pamaso pa munthuyo tikapanda kupita naye.’+
15 Chabwino, ndikuyesani motere kuti ndione ngati mukunena zoona: Simuchoka kuno mpaka mng’ono wanuyo atabwera,+ ndithu pali Farao wamoyo!
26 Koma ife tinati, ‘Sitingathe kutsikira kumeneko. Ngati tikhala naye limodzi mng’ono wathuyu tipitako, chifukwa sitingathe kukaonekeranso pamaso pa munthuyo tikapanda kupita naye.’+