Genesis 42:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiye ndikuyesani kuti ndione ngati mukunena zoona: Pali Farao wamoyo, ndithu simuchoka kuno mpaka mngʼono wanuyo atabwera.+
15 Ndiye ndikuyesani kuti ndione ngati mukunena zoona: Pali Farao wamoyo, ndithu simuchoka kuno mpaka mngʼono wanuyo atabwera.+