-
Genesis 42:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Mukabweretse mʼbale wanu wamngʼonoyo kwa ine kuti ndidzatsimikize kuti si inu akazitape koma anthu achilungamo. Mukatero, ndidzakubwezerani mʼbale wanuyu, ndipo mudzatha kuchita malonda mʼdziko lino.’”
-