Genesis 42:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mukabweretse m’bale wanu wamng’onoyo kwa ine kuti ndidzatsimikize kuti si inu akazitape koma anthu achilungamo. Mukadzatero, ndidzakubwezerani m’bale wanuyu, ndipo mudzatha kuchita malonda m’dziko lino.’”+
34 Mukabweretse m’bale wanu wamng’onoyo kwa ine kuti ndidzatsimikize kuti si inu akazitape koma anthu achilungamo. Mukadzatero, ndidzakubwezerani m’bale wanuyu, ndipo mudzatha kuchita malonda m’dziko lino.’”+