Rute 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova akudalitseni.+ Aliyense apeze mpumulo+ m’nyumba ya mwamuna wake.” Kenako anawapsompsona.+ Pamenepo iwo anayamba kulira mokweza mawu,
9 Yehova akudalitseni.+ Aliyense apeze mpumulo+ m’nyumba ya mwamuna wake.” Kenako anawapsompsona.+ Pamenepo iwo anayamba kulira mokweza mawu,