Genesis 47:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kumeneko, Yosefe anali kugawira chakudya bambo ake, abale ake ndi banja lonse la bambo ake,+ malinga ndi kuchuluka kwa ana.+ Miyambo 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+ Machitidwe 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero Yosefe anatumiza anthu ku Kanani kukatenga bambo ake Yakobo ndi achibale ake.+ Onse pamodzi analipo anthu 75.+
12 Kumeneko, Yosefe anali kugawira chakudya bambo ake, abale ake ndi banja lonse la bambo ake,+ malinga ndi kuchuluka kwa ana.+
27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+
14 Chotero Yosefe anatumiza anthu ku Kanani kukatenga bambo ake Yakobo ndi achibale ake.+ Onse pamodzi analipo anthu 75.+