Genesis 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nayenso Semu, kholo la ana onse a Ebere,+ anali ndi mbadwa zake. Semu anali mng’ono wake wa Yafeti, amene anali wamkulu pa onse. Genesis 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano iyi ndi mbiri ya Semu.+ Semu anali ndi zaka 100 pamene anabereka Aripakisadi,+ patapita zaka ziwiri pambuyo pa chigumula. Luka 3:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 mwana wa Kainani,mwana wa Aripakisadi,+mwana wa Semu,+mwana wa Nowa,+mwana wa Lameki,+
21 Nayenso Semu, kholo la ana onse a Ebere,+ anali ndi mbadwa zake. Semu anali mng’ono wake wa Yafeti, amene anali wamkulu pa onse.
10 Tsopano iyi ndi mbiri ya Semu.+ Semu anali ndi zaka 100 pamene anabereka Aripakisadi,+ patapita zaka ziwiri pambuyo pa chigumula.