Genesis 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’kupita kwa nthawi, Nowa anabereka ana aamuna atatu, Semu, Hamu ndi Yafeti.+ 1 Mbiri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nowa,+Semu,+ Hamu+ ndi Yafeti.+ Luka 3:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 mwana wa Kainani,mwana wa Aripakisadi,+mwana wa Semu,+mwana wa Nowa,+mwana wa Lameki,+