Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 5:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mwanayo anamutcha dzina lakuti Nowa,+ ndipo anati: “Uyu ndi amene adzatibweretsere mpumulo ku ntchito yathu yopweteketsa manja, chifukwa cholima nthaka imene Yehova anaitemberera.”+

  • Genesis 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma Nowa anayanjidwa ndi Yehova.

  • Yesaya 54:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Kwa ine, zimenezi zili ngati masiku a Nowa.+ Monga mmene ndinalumbirira kuti madzi a Nowa sadzadutsanso padziko lapansi,+ momwemonso ndalumbira kuti sindidzakukwiyira kapena kukudzudzula.+

  • Ezekieli 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Amuna atatu awa: Nowa,+ Danieli+ ndi Yobu,+ akanakhala m’dzikolo, iwo okhawo akanapulumutsa miyoyo yawo chifukwa chokhala olungama,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+

  • Mateyu 24:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Pakuti monga mmene analili masiku a Nowa,+ ndi mmenenso kukhalapo kwa Mwana wa munthu kudzakhalire.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena