Genesis 46:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamapeto pake Isiraeli anauza Yosefe kuti: “Ndingathe kufa+ tsopano chifukwa ndaona nkhope yako, popeza ukadali ndi moyo.” Luka 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Tsopano, Ambuye Wamkulu Koposa, mukulola kapolo wanu kupita mu mtendere+ malinga ndi zimene inu munanena.
30 Pamapeto pake Isiraeli anauza Yosefe kuti: “Ndingathe kufa+ tsopano chifukwa ndaona nkhope yako, popeza ukadali ndi moyo.”
29 “Tsopano, Ambuye Wamkulu Koposa, mukulola kapolo wanu kupita mu mtendere+ malinga ndi zimene inu munanena.