Genesis 45:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo Isiraeli anafuula kuti: “Basi, tsopano ndakhulupirira! Yosefe mwana wanga akadali ndi moyo! Ndipita ndikamuone ndisanafe!”+ Luka 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Tsopano, Ambuye Wamkulu Koposa, mukulola kapolo wanu kupita mu mtendere+ malinga ndi zimene inu munanena.
28 Pamenepo Isiraeli anafuula kuti: “Basi, tsopano ndakhulupirira! Yosefe mwana wanga akadali ndi moyo! Ndipita ndikamuone ndisanafe!”+
29 “Tsopano, Ambuye Wamkulu Koposa, mukulola kapolo wanu kupita mu mtendere+ malinga ndi zimene inu munanena.