Ekisodo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Awa ndi mayina a ana aamuna a Levi,+ malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo:+ Gerisoni, Kohati ndi Merari.+ Ndipo Levi anakhala ndi moyo zaka 137. Numeri 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mabanja a Agerisoni anali kukhala kumbuyo kwa chihema chopatulika.+ Anali kumanga msasa wawo kumadzulo.
16 Awa ndi mayina a ana aamuna a Levi,+ malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo:+ Gerisoni, Kohati ndi Merari.+ Ndipo Levi anakhala ndi moyo zaka 137.
23 Mabanja a Agerisoni anali kukhala kumbuyo kwa chihema chopatulika.+ Anali kumanga msasa wawo kumadzulo.