Genesis 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu anamuuzanso kuti: “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Ubereke ndipo ukhale ndi ana ambiri. Mitundu ndi mafuko ambiri adzatuluka mwa iwe, ndipo mafumu adzatuluka m’chiuno mwako.+
11 Mulungu anamuuzanso kuti: “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Ubereke ndipo ukhale ndi ana ambiri. Mitundu ndi mafuko ambiri adzatuluka mwa iwe, ndipo mafumu adzatuluka m’chiuno mwako.+