Yoweli 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ziweto zausa moyo. Gulu la ng’ombe likuyendayenda mosokonezeka pakuti kulibe msipu woti zidye.+ Ndiponso gulu la nkhosa ndi limene lalangidwa chifukwa cha uchimo.
18 Ziweto zausa moyo. Gulu la ng’ombe likuyendayenda mosokonezeka pakuti kulibe msipu woti zidye.+ Ndiponso gulu la nkhosa ndi limene lalangidwa chifukwa cha uchimo.