4 Kodi dzikoli lifotabe mpaka liti?+ Kodi zomera za m’minda yonse ziumabe mpaka liti?+ Chifukwa chakuti anthu a m’dzikoli ndi oipa, zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka zinachoka.+ Pakuti anthuwo akuti: “Iye sakuona zimene zidzatichitikira m’tsogolo.”