Genesis 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Patapita nthawi, Yakobo anafika bwinobwino kumzinda wa Sekemu,+ m’dziko la Kanani,+ akuchokera ku Padana-ramu.+ Atafika, anamanga msasa pafupi ndi mzindawo. Hoseya 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yakobo anathawira kumunda wa ku Siriya+ ndipo Isiraeli+ anapitirizabe kugwira ntchito+ ndi kulondera nkhosa kuti apeze mkazi.+
18 Patapita nthawi, Yakobo anafika bwinobwino kumzinda wa Sekemu,+ m’dziko la Kanani,+ akuchokera ku Padana-ramu.+ Atafika, anamanga msasa pafupi ndi mzindawo.
12 Yakobo anathawira kumunda wa ku Siriya+ ndipo Isiraeli+ anapitirizabe kugwira ntchito+ ndi kulondera nkhosa kuti apeze mkazi.+