12 Tsopano Davide anali mwana wamwamuna wa Jese, Mwefurata+ wina wa ku Betelehemu, ku Yuda. Jese anali ndi ana aamuna 8+ ndipo m’masiku a Sauli iye anali atakalamba kale.
6 ‘Iwe Betelehemu+ wa m’dziko la Yuda, suli mzinda waung’ono kwambiri kwa olamulira a Yuda, chifukwa mwa iwe mudzatuluka wolamulira+ amene adzaweta+ anthu anga, Aisiraeli.’”