Genesis 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atakweza maso,+ anaona amuna atatu ataima chapatali ndi iye. Atawaona, ananyamuka pakhomo la hemayo n’kuthamanga kukakumana nawo. Atafika, anagwada n’kuwaweramira mpaka nkhope yake pansi.+ Genesis 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma iyeyo anapita patsogolo pawo, n’kuyamba kugwada, n’kumaweramitsa nkhope yake pansi mpaka nthawi 7. Anachita zimenezi mpaka kufika pafupi ndi m’bale wakeyo.+
2 Atakweza maso,+ anaona amuna atatu ataima chapatali ndi iye. Atawaona, ananyamuka pakhomo la hemayo n’kuthamanga kukakumana nawo. Atafika, anagwada n’kuwaweramira mpaka nkhope yake pansi.+
3 Koma iyeyo anapita patsogolo pawo, n’kuyamba kugwada, n’kumaweramitsa nkhope yake pansi mpaka nthawi 7. Anachita zimenezi mpaka kufika pafupi ndi m’bale wakeyo.+