Genesis 49:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Onsewa ndiwo mafuko 12 a Isiraeli, ndipo izi n’zimene bambo awo analankhula kwa iwo powadalitsa. Anapatsa aliyense wa iwo madalitso ake omuyenerera.+
28 Onsewa ndiwo mafuko 12 a Isiraeli, ndipo izi n’zimene bambo awo analankhula kwa iwo powadalitsa. Anapatsa aliyense wa iwo madalitso ake omuyenerera.+