Deuteronomo 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kwa Zebuloni anati:+“Kondwera Zebuloni iwe, pa maulendo ako,+Ndiponso iwe Isakara, m’mahema ako.+ Yoswa 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maere achinayi anagwera Isakara,+ kapena kuti ana a Isakara potsata mabanja awo. 1 Mbiri 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Abale awo a mabanja onse a Isakara, anali amuna amphamvu ndi olimba mtima+ okwana 87,000 pamndandanda wa mayina awo onse wotsatira makolo awo.+
5 Abale awo a mabanja onse a Isakara, anali amuna amphamvu ndi olimba mtima+ okwana 87,000 pamndandanda wa mayina awo onse wotsatira makolo awo.+