Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 49:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Isakara+ ndi bulu wa mafupa olimba, amagona pansi atasenza matumba a katundu uku ndi uku.

  • Numeri 33:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Mukagawire dzikolo kwa mabanja anu monga cholowa chanu mwa kuchita maere.+ Banja la anthu ambiri mukaliwonjezere cholowa chawo, ndipo banja la anthu ochepa mukalichepetsere cholowa chawo.+ Malo alionse amene maere akagwere banja, akapatsidwe kwa banjalo.+ Mukagawane malowo potsata mafuko a makolo anu.+

  • Deuteronomo 33:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kwa Zebuloni anati:+

      “Kondwera Zebuloni iwe, pa maulendo ako,+

      Ndiponso iwe Isakara, m’mahema ako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena