Mlaliki 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndi bwino kupita kunyumba yamaliro kusiyana ndi kupita kunyumba yamadyerero,+ chifukwa amenewo ndiwo mapeto a anthu onse. Chotero munthu amene ali moyo aziganizira zimenezi mumtima mwake. Yohane 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yesu anagwetsa misozi.+ Machitidwe 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amuna ena oopa Mulungu anatenga Sitefano ndi kukamuika m’manda,+ ndipo anamulira kwambiri.+
2 Ndi bwino kupita kunyumba yamaliro kusiyana ndi kupita kunyumba yamadyerero,+ chifukwa amenewo ndiwo mapeto a anthu onse. Chotero munthu amene ali moyo aziganizira zimenezi mumtima mwake.