Genesis 47:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Yakobo anati: “Lumbira kwa ine.” Yosefe analumbira kwa iye.+ Pamenepo Isiraeli anawerama n’kutsamira kumutu kwa bedi lake.+ Mateyu 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Komanso munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti, ‘Usamalumbire+ koma osachita, m’malomwake uzikwaniritsa malonjezo ako kwa Yehova.’+ Aheberi 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti anthu polumbira amatchula winawake wamkulu kwa iwo,+ ndipo lumbiro lawo limathetsa mkangano uliwonse, chifukwa kwa iwo lumbiro ndi chotsimikizira chalamulo.+
31 Ndiyeno Yakobo anati: “Lumbira kwa ine.” Yosefe analumbira kwa iye.+ Pamenepo Isiraeli anawerama n’kutsamira kumutu kwa bedi lake.+
33 “Komanso munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti, ‘Usamalumbire+ koma osachita, m’malomwake uzikwaniritsa malonjezo ako kwa Yehova.’+
16 Pakuti anthu polumbira amatchula winawake wamkulu kwa iwo,+ ndipo lumbiro lawo limathetsa mkangano uliwonse, chifukwa kwa iwo lumbiro ndi chotsimikizira chalamulo.+