1 Mafumu 1:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Kuwonjezera apo, atumiki a mfumu abwera kudzafunira mafuno abwino mbuye wathu Mfumu Davide kuti: ‘Mulungu wanu akulitse dzina la Solomo kuposa dzina lanu ndiponso akweze ufumu wake kuposa ufumu wanu!’+ Kenako mfumuyo inaweramira pabedi.+ Aheberi 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwa chikhulupiriro, Yakobo ali pafupi kufa,+ anadalitsa ana aamuna a Yosefe mmodzimmodzi,+ ndipo analambira Mulungu atatsamira pamutu wa ndodo yake.+
47 Kuwonjezera apo, atumiki a mfumu abwera kudzafunira mafuno abwino mbuye wathu Mfumu Davide kuti: ‘Mulungu wanu akulitse dzina la Solomo kuposa dzina lanu ndiponso akweze ufumu wake kuposa ufumu wanu!’+ Kenako mfumuyo inaweramira pabedi.+
21 Mwa chikhulupiriro, Yakobo ali pafupi kufa,+ anadalitsa ana aamuna a Yosefe mmodzimmodzi,+ ndipo analambira Mulungu atatsamira pamutu wa ndodo yake.+