Genesis 47:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Yakobo anati: “Lumbira kwa ine.” Yosefe analumbira kwa iye.+ Pamenepo Isiraeli anawerama n’kutsamira kumutu kwa bedi lake.+ Aheberi 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwa chikhulupiriro, Yakobo ali pafupi kufa,+ anadalitsa ana aamuna a Yosefe mmodzimmodzi,+ ndipo analambira Mulungu atatsamira pamutu wa ndodo yake.+
31 Ndiyeno Yakobo anati: “Lumbira kwa ine.” Yosefe analumbira kwa iye.+ Pamenepo Isiraeli anawerama n’kutsamira kumutu kwa bedi lake.+
21 Mwa chikhulupiriro, Yakobo ali pafupi kufa,+ anadalitsa ana aamuna a Yosefe mmodzimmodzi,+ ndipo analambira Mulungu atatsamira pamutu wa ndodo yake.+