Aheberi 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa cha chikhulupiriro, Yakobo atatsala pangʼono kumwalira,+ anadalitsa ana aamuna a Yosefe mmodzimmodzi,+ ndipo kenako analambira Mulungu atatsamira ndodo yake.+
21 Chifukwa cha chikhulupiriro, Yakobo atatsala pangʼono kumwalira,+ anadalitsa ana aamuna a Yosefe mmodzimmodzi,+ ndipo kenako analambira Mulungu atatsamira ndodo yake.+