1 Mafumu 1:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Monga momwe Yehova anakhalira ndi inu mbuyanga mfumu,+ akhalenso ndi Solomo+ ndipo achititse mpando wake wachifumu kukhala waukulu+ kuposa mpando wanu wachifumu, mbuyanga Mfumu Davide.” Luka 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iwo anali kunena kuti: “Wodalitsidwa Iye wobwera monga Mfumu m’dzina la Yehova!+ Mtendere kumwamba, ndi ulemerero kumwambamwambako!”+
37 Monga momwe Yehova anakhalira ndi inu mbuyanga mfumu,+ akhalenso ndi Solomo+ ndipo achititse mpando wake wachifumu kukhala waukulu+ kuposa mpando wanu wachifumu, mbuyanga Mfumu Davide.”
38 Iwo anali kunena kuti: “Wodalitsidwa Iye wobwera monga Mfumu m’dzina la Yehova!+ Mtendere kumwamba, ndi ulemerero kumwambamwambako!”+