Genesis 48:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Isiraeli atatero, anauza Yosefe kuti: “Taona, inetu ndikufa.+ Koma Mulungu adzakhalabe nanu ndithu anthu inu, ndipo adzakubwezerani kudziko la makolo anu.+ 1 Akorinto 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti monga mwa Adamu onse akufa,+ momwemonso mwa Khristu onse adzapatsidwa+ moyo.
21 Isiraeli atatero, anauza Yosefe kuti: “Taona, inetu ndikufa.+ Koma Mulungu adzakhalabe nanu ndithu anthu inu, ndipo adzakubwezerani kudziko la makolo anu.+