Genesis 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinalota tikumanga mitolo ya tirigu pakati pa munda. Mtolo wanga unadzuka n’kuima chilili. Mitolo yanunso inadzuka, ndipo inazungulira mtolo wanga n’kuyamba kuuweramira.”+ Aefeso 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khalani akapolo amaganizo abwino, monga otumikira Yehova+ osati anthu,
7 Ndinalota tikumanga mitolo ya tirigu pakati pa munda. Mtolo wanga unadzuka n’kuima chilili. Mitolo yanunso inadzuka, ndipo inazungulira mtolo wanga n’kuyamba kuuweramira.”+