Genesis 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nthaka ya padziko lapansi inali isanayambe kumera zitsamba ndi zomera zina, chifukwa Yehova Mulungu anali asanagwetse mvula+ padziko lapansi. Panalibenso munthu woti n’kulima nthakayo. Yobu 37:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa chipale chofewa amachiuza kuti, ‘Gwera padziko lapansi.’+Amauzanso mvula zimenezi, ngakhalenso mvula yamphamvu ikamakhuthuka.+
5 Nthaka ya padziko lapansi inali isanayambe kumera zitsamba ndi zomera zina, chifukwa Yehova Mulungu anali asanagwetse mvula+ padziko lapansi. Panalibenso munthu woti n’kulima nthakayo.
6 Chifukwa chipale chofewa amachiuza kuti, ‘Gwera padziko lapansi.’+Amauzanso mvula zimenezi, ngakhalenso mvula yamphamvu ikamakhuthuka.+