Yobu 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amaletsa madzi ndipo amauma,+Amawatumiza ndipo madziwo amasintha dziko lapansi.+ 2 Petulo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ndipo mwa zimenezi, dziko la pa nthawiyo linawonongedwa pamene linamizidwa ndi madzi.+