Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 7:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 M’chaka cha 600 cha moyo wa Nowa, m’mwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli akasupe onse amadzi akuya* anaphulika ndipo zotsekera madzi akumwamba zinatseguka.+

  • Genesis 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Chotero, Mulungu anaseseratu chamoyo chilichonse chimene chinali padziko lapansi, kuyambira munthu mpaka nyama, zokwawa pansi mpaka zolengedwa zouluka m’mlengalenga, anazisesa zonse padziko lapansi.+ Koma Nowa yekha, pamodzi ndi amene anali naye limodzi m’chingalawacho, anapulumuka.+

  • Yesaya 54:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Kwa ine, zimenezi zili ngati masiku a Nowa.+ Monga mmene ndinalumbirira kuti madzi a Nowa sadzadutsanso padziko lapansi,+ momwemonso ndalumbira kuti sindidzakukwiyira kapena kukudzudzula.+

  • Mateyu 24:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Anthu ananyalanyaza zimene zinali kuchitika mpaka chigumula chinafika n’kuwaseseratu onsewo.+ Zidzateronso ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena