Genesis 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zamoyo zamtundu uliwonse, zokhala ndi mphamvu ya moyo+ m’thupi mwawo, zinali kupita ziwiriziwiri m’chingalawa mmene munali Nowa. 1 Akorinto 15:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mnofu sukhala wa mtundu umodzi, koma pali mnofu wa munthu, ndipo pali wa nyama, palinso wa mbalame, ndi winanso wa nsomba.+
15 Zamoyo zamtundu uliwonse, zokhala ndi mphamvu ya moyo+ m’thupi mwawo, zinali kupita ziwiriziwiri m’chingalawa mmene munali Nowa.
39 Mnofu sukhala wa mtundu umodzi, koma pali mnofu wa munthu, ndipo pali wa nyama, palinso wa mbalame, ndi winanso wa nsomba.+