Genesis 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Motero Mulungu anapanga nyama zakutchire monga mwa mitundu yake. Anapanganso nyama zoweta monga mwa mitundu yake, komanso nyama iliyonse yokwawa panthaka monga mwa mtundu wake.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.
25 Motero Mulungu anapanga nyama zakutchire monga mwa mitundu yake. Anapanganso nyama zoweta monga mwa mitundu yake, komanso nyama iliyonse yokwawa panthaka monga mwa mtundu wake.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.